2 Samueli 7:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali pakukhala mfumuyo m'nyumba mwake, atampumulitsa Yehova pa adani ake onse omzungulira, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali pakukhala mfumuyo m'nyumba mwake, atampumulitsa Yehova pa adani ake onse omzungulira, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Nthaŵi imene mfumu Davide anali atakhazikika m'nyumba mwake, Chauta adampumuza kwa adani ake onse omzungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mfumu itakhazikika mʼnyumba yake yaufumu, Yehova atayipatsa mpumulo kwa adani ake onse woyizungulira, Onani mutuwo |