2 Samueli 6:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo kudaipira Davide, chifukwa Yehova anachita chipasulo ndi Uza; natcha malowo Pereziuza, kufikira lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo kudaipira Davide, chifukwa Yehova anachita chipasulo ndi Uza; natcha malowo Pereziuza, kufikira lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Davide adakhumudwa chifukwa chakuti Chauta adaakantha Uza. Ndipo mpaka pano malo amenewo amaŵatchula kuti Pereziuza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndipo Davide anakhumudwa chifukwa Yehova anakantha Uza ndipo mpaka lero malowo amatchedwa Perezi Uza. Onani mutuwo |