2 Samueli 6:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Davide anaopa Yehova tsiku lomwelo; nati, Ngati likasa la Yehova lidzafika kwa ine? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Davide anaopa Yehova tsiku lomwelo; nati, Ngati likasa la Yehova lidzafika kwa ine? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Davide adachita mantha ndi Chauta tsiku limenelo, ndipo adafunsa kuti, “Kodi Bokosi la Chautali lingafike bwanji kwathu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Tsiku limenelo Davide anachita mantha ndi Yehova ndipo anati, “Kodi Bokosi la Yehova lingafike bwanji kwathu?” Onani mutuwo |