Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 6:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ndipo Davide anakhumudwa chifukwa Yehova anakantha Uza ndipo mpaka lero malowo amatchedwa Perezi Uza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Ndipo kudaipira Davide, chifukwa Yehova anachita chipasulo ndi Uza; natcha malowo Pereziuza, kufikira lero lino.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo kudaipira Davide, chifukwa Yehova anachita chipasulo ndi Uza; natcha malowo Pereziuza, kufikira lero lino.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tsono Davide adakhumudwa chifukwa chakuti Chauta adaakantha Uza. Ndipo mpaka pano malo amenewo amaŵatchula kuti Pereziuza.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 6:8
6 Mawu Ofanana  

Yehova anapsera mtima Uza chifukwa chochita chinthu chosayenera kuchitika. Choncho Mulungu anamukantha ndipo anafera pomwepo pambali pa Bokosi la Mulungulo.


Tsiku limenelo Davide anachita mantha ndi Yehova ndipo anati, “Kodi Bokosi la Yehova lingafike bwanji kwathu?”


Popeza kuti inu Alevi simunalinyamule poyamba paja, Yehova Mulungu wathu anatikantha. Sitinafunse momwe tikanachitira monga mmene Iyeyo anafotokozera.”


Koma Yona anakhumudwa kwambiri ndipo anakwiya.


Koma Mulungu anati kwa Yona, “Kodi nʼkoyenera kuti iwe ukwiye chifukwa cha msatsi?” Iye anayankha kuti, “Inde nʼkoyenera. Kukwiya kwanga nʼkofuna kufa nako.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa