2 Samueli 6:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Davide anavina ndi mphamvu yake yonse pamaso pa Yehova; Davide nadzimangirira efodi wabafuta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Davide anavina ndi mphamvu yake yonse pamaso pa Yehova; Davide nadzimangirira efodi wabafuta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Davide atavala efodi yabafuta ankavina molemekeza Chauta ndi mphamvu zake zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Davide ankavina ndi mphamvu zake zonse pamaso pa Yehova atavala efodi ya nsalu yofewa yosalala, Onani mutuwo |