2 Samueli 6:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo kunali, pamene akunyamula likasa la Yehova atayenda mapazi asanu ndi limodzi, iye anapha nsembe ng'ombe ndi chonenepa china. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo kunali, pamene akunyamula likasa la Yehova atayenda mapazi asanu ndi limodzi, iye anapha nsembe ng'ombe ndi chonenepa china. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndipo anthu amene ankanyamula Bokosi lachipanganolo ankati akayenda mapazi asanu ndi limodzi, Davide ankapereka nsembe ya ng'ombe yamphongo ndi mwanawang'ombe wonenepa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Anthu amene ananyamula Bokosi la Yehova ankati akayenda mapazi asanu ndi limodzi, iye ankapereka nsembe ngʼombe yayimuna ndi mwana wangʼombe wonenepa. Onani mutuwo |