2 Samueli 6:1 - Buku Lopatulika1 Pambuyo pake Davide anamemezanso osankhika onse a mu Israele, anthu zikwi makumi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pambuyo pake Davide anamemezanso osankhika onse a m'Israele, anthu zikwi makumi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Davide adasonkhanitsanso ankhondo okwanira 30,000, amene adaŵasankha pakati pa Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Davide anasonkhanitsanso pamodzi ankhondo 3,000 osankhidwa pakati pa Aisraeli. Onani mutuwo |