Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 6:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Davide anasonkhanitsanso pamodzi ankhondo 3,000 osankhidwa pakati pa Aisraeli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

1 Pambuyo pake Davide anamemezanso osankhika onse a mu Israele, anthu zikwi makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Pambuyo pake Davide anamemezanso osankhika onse a m'Israele, anthu zikwi makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Davide adasonkhanitsanso ankhondo okwanira 30,000, amene adaŵasankha pakati pa Aisraele.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 6:1
7 Mawu Ofanana  

Sindidzalandira kanthu kalikonse kupatula zokhazo zimene anthu anga adya ndi gawo la katundu la anthu amene ndinapita nawo monga Aneri, Esikolo ndi Mamre. Iwowa atenge gawo lawo.”


Mafuko onse a Israeli anabwera kwa Davide ku Hebroni ndipo anati, “Ife ndife mafupa ndi mnofu wanu.


Pamenepo Mfumu Solomoni inasonkhanitsa akuluakulu a Israeli, atsogoleri onse a mafuko ndi akuluakulu a mabanja a Aisraeli mu Yerusalemu, kuti akatenge Bokosi la Chipangano la Yehova ku Ziyoni, Mzinda wa Davide.


Kotero Davide anasonkhanitsa Aisraeli onse, kuchokera ku mtsinje wa Sihori ku Igupto mpaka ku Lebo Hamati, kuti abweretse Bokosi la Mulungu kuchokera ku Kiriati-Yearimu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa