Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 5:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo Davide anatero, monga Yehova anamlamulira, nakantha Afilisti kuyambira ku Geba kufikira ku Gezere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo Davide anatero, monga Yehova anamlamulira, nakantha Afilisti kuyambira ku Geba kufikira ku Gezere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Davide adachitadi monga momwe Chauta adaamlamulira, ndipo adagonjetsa Afilistiwo kuyambira ku Geba mpaka ku Gezere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Kotero Davide anachita zimene Yehova anamulamulira ndipo anakantha Afilisti njira yonse kuchokera ku Geba mpaka ku Gezeri.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 5:25
9 Mawu Ofanana  

Ndipo m'tsogolo mwake Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa Davide nalanda mudzi wa Metege Ama m'manja mwa Afilisti.


Nachita Davide monga Mulungu adamuuza, nakantha gulu la Afilisti kuyambira ku Gibiyoni kufikira ku Gezere.


Ndipo anthu anawerama, nalambira. Ndipo ana a Israele anamuka nachita monga Yehova adalamulira Mose ndi Aroni; anachita momwemo.


Pakuti Yehova adzauka monga m'phiri la Perazimu, nadzakwiya monga m'chigwa cha Gibiyoni; kuti agwire ntchito yake, ntchito yake yachilendo, ndi kuti achite chochita chake, chochita chake chachilendo.


Pamenepo Horamu mfumu ya Gezere anakwera kudzathandiza Lakisi; ndipo Yoswa anamkantha iye ndi anthu ake mpaka sanamsiyire ndi mmodzi yense.


mfumu ya ku Egiloni, imodzi; mfumu ya ku Gezere, imodzi;


Ndipo sanaingitse Akanani akukhala mu Gezere; koma Akanani anakhala pakati pa Efuremu, kufikira lero lino, nawaumiriza kugwira ntchito yathangata.


ndi Kefaramoni, ndi Ofini, ndi Geba; mizinda khumi ndi iwiri pamodzi ndi midzi yao;


Ndipo anawapatsa Sekemu ndi mabusa ake ku mapiri a Efuremu, ndiwo mzinda wopulumukirako wakupha mnzakeyo, ndi Gezere ndi mabusa ake;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa