2 Samueli 5:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo kudzali, pakumva iwe kuwayula ku nsonga za mkandankhuku, pomwepo fulumiratu, pakuti pamenepo Yehova watuluka pamaso pako kukakantha khamu la Afilisti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo kudzali, pakumva iwe kuwayula ku nsonga za mkandankhuku, pomwepo fulumiratu, pakuti pamenepo Yehova watuluka pamaso pako kukakantha khamu la Afilisti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsono ukakamva phokoso pa nsonga za mitengo ya mkandankhukuyo, pamenepo ukakonzeke, chifukwa ndiye kuti Chauta wakutsogolera kuti ukakanthe gulu lankhondo la Afilistiwo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Mukakangomva phokoso pa msonga za mitengo ya mkandankhuku, mukayende mofulumira, chifukwa izi zikasonyeza kuti Yehova ali patsogolo panu kukantha ankhondo a Afilisti.” Onani mutuwo |