2 Samueli 4:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo pamene Isiboseti mwana wa Saulo, anamva kuti Abinere adakafera ku Hebroni, manja ake anafooka, ndi Aisraele onse anavutika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo pamene Isiboseti mwana wa Saulo, anamva kuti Abinere adakafera ku Hebroni, manja ake anafooka, ndi Aisraele onse anavutika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Isiboseti, mwana wa Saulo, atamva kuti Abinere adakafera ku Hebroni, adataya mtima, ndipo Aisraele onse adachita mantha kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Isiboseti mwana wa Sauli atamva kuti Abineri waphedwa ku Hebroni, anataya mtima ndipo Aisraeli onse anachita mantha kwambiri. Onani mutuwo |