2 Samueli 3:9 - Buku Lopatulika9 Mulungu alange Abinere, naonjezepo, ndikapanda kumchitira Davide monga Yehova anamlumbirira; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mulungu alange Abinere, naonjezepo, ndikapanda kumchitira Davide monga Yehova anamlumbirira; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Nchifukwa chake Mulungu andilange, ngakhale kundipha kumene, ngati sindimchitira Davide zimene Chauta adamlonjeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mulungu andilange ine Abineri, andilange kwambiri, ngati sindichitira Davide zimene Yehova anamulonjeza iye mwa lumbiro. Onani mutuwo |