2 Samueli 3:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo mfumu inati kwa anyamata ake, Simudziwe kodi kuti kalonga ndi munthu womveka wagwa lero mu Israele? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo mfumu inati kwa anyamata ake, Simudziwa kodi kuti kalonga, ndi munthu womveka, wagwa lero m'Israele? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Ndipo mfumu Davide adafunsa ankhondo ake kuti, “Kodi simukudziŵa kuti lero m'dziko la Israele mwagwa kalonga amene ali munthu wamkulu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Ndipo mfumu inati kwa ankhondo ake, “Kodi inu simukudziwa kuti lero mu Israeli mwagwa kalonga ndi munthu wamkulu? Onani mutuwo |