2 Samueli 3:37 - Buku Lopatulika37 Momwemo anthu onse ndi Aisraele onse anazindikira tsiku lija kuti sikunafumire kwa mfumu kupha Abinere mwana wa Nere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Momwemo anthu onse ndi Aisraele onse anazindikira tsiku lija kuti sikunafumira kwa mfumu kupha Abinere mwana wa Nere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Choncho onse amene ankakhala ndi mfumu pamodzi ndi Aisraele onse adamvetsa tsiku limenelo kuti sikunali kufuna kwa mfumu kuti Abinere mwana wa Nere aphedwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Kotero tsiku limeneli anthu onse ndi Aisraeli onse anadziwa kuti sikunali kufuna kwa mfumu kuti Abineri mwana wa Neri aphedwe. Onani mutuwo |
Ndipo Yehova adzambwezera mwazi wake pamutu wake wa iye yekha, popeza iye anawakantha anthu awiri olungama ndi okoma oposa iye mwini, nawapha ndi lupanga, atate wanga Davide osadziwa, ndiwo Abinere mwana wa Nere kazembe wa khamu la nkhondo la Israele, ndi Amasa mwana wa Yetere kazembe wa khamu la nkhondo la Yuda.