Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 3:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo anthu onse anachisamalira, ndipo chinawakomera; zilizonse adazichita mfumu zidakomera anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo anthu onse anachisamalira, ndipo chinawakomera; zilizonse adazichita mfumu zidakomera anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Anthu onse adamvera zimenezo, ndipo zidaŵakomera. Zonse zimene ankachita mfumu zinkaŵakondwetsa anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Anthu onse anadziwa zimenezi ndipo zinawakondweretsa ndithu. Zonse zimene mfumu inachita zinawakondweretsa.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 3:36
7 Mawu Ofanana  

Ndipo mthenga unafika kwa Davide nuti, Mitima ya anthu a Israele itsata Abisalomu.


Abisalomu anachitira zotero Aisraele onse akudza kwa mfumu kuti aweruze mlandu wao; chomwecho Abisalomu anakopa mitima ya anthu a Israele.


Ndipo anthu onse anadza kudzadyetsa Davide chakudya kukali msana; koma Davide analumbira nati, Mulungu andilange naonjezepo, ngati ndilawa mkate kapena kanthu kena, lisanalowe dzuwa.


Momwemo anthu onse ndi Aisraele onse anazindikira tsiku lija kuti sikunafumire kwa mfumu kupha Abinere mwana wa Nere.


Indetu, anthu achabe ndi mpweya, ndipo anthu aakulu ndi bodza, pakuwayesa apepuka; onse pamodzi apepuka koposa mpweya.


Ndipo anadabwa kwakukulukulu, nanena, Wachita Iye zonse bwino; angakhale ogontha awamvetsa, ndi osalankhula awalankhulitsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa