2 Samueli 3:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo pambuyo pake, pakuchimva Davide, anati, Ine ndi ufumu wanga tikhala osachimwira mwazi wa Abinere mwana wa Nere, nthawi zonse, pamaso pa Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo pambuyo pake, pakuchimva Davide, anati, Ine ndi ufumu wanga tikhala osachimwira mwazi wa Abinere mwana wa Nere, nthawi zonse, pamaso pa Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Pambuyo pake Davide atamva, adati, “Ine pamodzi ndi anthu a mu ufumu wanga tilibe ndi mlandu womwe pamaso pa Chauta pa imfa ya Abinere, mwana wa Nere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Patapita nthawi, Davide atamva zimenezi anati, “Ine ndi ufumu wanga tidzakhala osalakwa pamaso pa Yehova pa imfa ya Abineri mwana wa Neri. Onani mutuwo |