2 Samueli 3:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Yowabu anatuluka kwa Davide, natumizira Abinere mithenga, amene anambweza ku chitsime cha Sira. Koma Davide sanachidziwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Yowabu anatuluka kwa Davide, natumizira Abinere mithenga, amene anambweza ku chitsime cha Sira. Koma Davide sanachidziwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Yowabu atachokako kwa Davide kuja, adatuma amithenga kuti amlondole Abinere. Iwowo adakampezadi ku chitsime cha Sira, nambweza, Davide osadziŵa kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Kenaka Yowabu anachoka pamaso pa Davide ndipo anatumiza amithenga kutsatira Abineri, ndipo anabwera naye kuchokera ku chitsime cha Sira. Koma Davide sanadziwe zimenezi. Onani mutuwo |