Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 3:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo iye sanakhoze kuyankha Abinere mau amodzi chifukwa cha kumuopa iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo iye sanakhoze kuyankha Abinere mau amodzi chifukwa cha kumuopa iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Pamenepo Isiboseti adangoti kukamwa yasa, osatha kumuyankha Abinere mau ndi amodzi omwe, chifukwa ankamuwopa kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Isiboseti sanayerekezenso kunena mawu ena kwa Abineri, chifukwa ankamuopa.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 3:11
3 Mawu Ofanana  

kuchotsa ufumu kunyumba ya Saulo ndi kukhazika mpando wachifumu wa Davide pa Israele ndi pa Yuda, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba.


Ndipo Abinere anatuma mithenga imnenere kwa Davide, nati, Dziko nla yani? Natinso, Mupangane nane pangano lanu, ndipo onani, ndidzagwirizana nanu ndi kukopa Aisraele onse atsate inu.


Mwagwedeza dziko, mwaling'amba. Konzani ming'alu yake; pakuti ligwedezeka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa