2 Samueli 23:7 - Buku Lopatulika7 koma wakukhudza iyo adzikonzeratu chitsulo ndi luti la mkondo; ndipo idzatenthedwa konse ndi moto m'malo mwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 koma wakukhudza iyo adzikonzeratu chitsulo ndi luti la mkondo; ndipo idzatenthedwa konse ndi moto m'malo mwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma amaidula ndi chigwandali nakaitentha pa moto.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Aliyense amene wayikhudza mingayo amayidula pogwiritsa ntchito chigwandali kapena ndodo ya mkondo; nayitentha pa moto.” Onani mutuwo |