2 Samueli 23:6 - Buku Lopatulika6 Koma oipa onse adzakhala ngati minga yoyenera kuitaya, pakuti siigwiridwa ndi dzanja; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma oipa onse adzakhala ngati minga yoyenera kuitaya, pakuti siigwiridwa ndi dzanja; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma anthu oipa onse amachotsedwa ngati minga. Anthu satha kuigwira ndi manja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma anthu oyipa ndiwo ayenera kutayidwa kunja ngati minga, imene sitengedwa ndi manja. Onani mutuwo |