2 Samueli 23:22 - Buku Lopatulika22 Izi anachita Benaya mwana wa Yehoyada, natenga dzina mwa ngwazi zitatuzo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Izi anachita Benaya mwana wa Yehoyada, natenga dzina mwa ngwazi zitatuzo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Zimenezi ndi ntchito zimene adatchuka nazo Benaya mwana wa Yehoyada, yemwe anali m'modzi wa anthu makumi atatu amphamvu aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Izi ndi zamphamvu zimene Benaya mwana wa Yehoyada anachita. Iyeyo analinso wotchuka ngati anthu atatu amphamvu aja. Onani mutuwo |