2 Samueli 23:23 - Buku Lopatulika23 Iye ndiye waulemu koposa makumi atatuwo, koma sadafikane ndi atatu oyamba. Ndipo Davide anamuika kuyang'anira olindirira ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Iye ndiye waulemu koposa makumi atatuwo, koma sadafikana ndi atatu oyamba. Ndipo Davide anamuika kuyang'anira olindirira ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Iyeyo anali womveka pakati pa atsogoleri makumi atatu aja, komabe sadafikepo pa anthu atatu aja. Davide adamuika kuti azilamulira asilikali ake omuteteza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Iye ankalemekezedwa kuposa wina aliyense mwa anthu makumi atatu aja, koma sanali mʼgulu la anthu atatu aja. Ndipo Davide anamuyika kukhala woyangʼanira asilikali omuteteza. Onani mutuwo |