2 Samueli 23:24 - Buku Lopatulika24 Asahele mbale wa Yowabu anali wa makumi atatuwo; Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Asahele mbale wa Yowabu anali wa makumi atatuwo; Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 M'gulu la anthu makumi atatu aja munalinso aŵa: Asahele, mbale wa Yowabu, Elihanani, mwana wa Dodo, wa ku Betelehemu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Mʼgulu la anthu makumi atatu aja munalinso awa: Asaheli mʼbale wa Yowabu, Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu, Onani mutuwo |