2 Samueli 23:19 - Buku Lopatulika19 Kodi iye sindiye waulemu mwa atatuwa? Chifukwa chake anali kazembe wao; ngakhale iyenso sadafikane ndi atatu oyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Kodi iye sindiye waulemu mwa atatuwa? Chifukwa chake anali kazembe wao; ngakhale iyenso sadafikana ndi atatu oyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Iyeyo anali womveka kwambiri mwa atsogoleri makumi atatu aja, ndipo adasanduka mkulu wao. Komabe sadafikepo pa anthu atatu aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Kodi iyeyo sanali wolemekezeka koposa? Iye anakhala mtsogoleri wawo ngakhale kuti sanali mʼgulu la anthu atatu aja. Onani mutuwo |