2 Samueli 22:4 - Buku Lopatulika4 Ndidzaitana kwa Yehova amene ayenera timtamande; chomwecho ndidzapulumutsidwa kwa adani anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndidzaitana kwa Yehova amene ayenera timtamande; chomwecho ndidzapulumutsidwa kwa adani anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndimaitana Chauta, amene ayenera kumtamanda, ndipo amandipulumutsa kwa adani anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Ndimayitana Yehova amene ndi woyenera matamando, ndipo ndapulumutsidwa kwa adani anga. Onani mutuwo |