2 Samueli 21:22 - Buku Lopatulika22 Awa anai anawabala ndi Rafa ku Gati; ndipo anagwa ndi dzanja la Davide ndi la anyamata ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Awa anai anawabala ndi Rafa ku Gati; ndipo anagwa ndi dzanja la Davide ndi la anyamata ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Anthu anaiwo anali zidzukulu za Arefaimu a ku Gati, ndipo adaphedwa ndi Davide ndi ankhondo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Anthu anayi amenewa anali zidzukulu za Rafa ku Gati, ndipo onse anaphedwa ndi Davide ndi ankhondo ake. Onani mutuwo |