2 Samueli 21:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo pakutonza Israele iyeyu, Yonatani mwana a Simea mbale wa Davide anamupha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo pakutonza Israele iyeyu, Yonatani mwana a Simea mbale wa Davide anamupha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pamene iye ankanyoza Aisraele, Yonatani mwana wa Simea, mbale wa Davide, adamupha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pamene iye ankanyoza Aisraeli, Yonatani mwana wa Simea, mʼbale wake wa Davide anamupha. Onani mutuwo |