Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 21:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo anauza Davide chimene Rizipa mwana wamkazi wa Aya, mkazi wamng'ono wa Saulo anachita.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo anauza Davide chimene Rizipa mwana wamkazi wa Aya, mkazi wamng'ono wa Saulo anachita.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Davide atamva zimene Rizipa mwana wa Aya, mzikazi wa Saulo adachita,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Davide atawuzidwa zimene Rizipa mwana wamkazi wa Ayiwa, mzikazi wa Sauli anachita,

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 21:11
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anthu Ayuda anabwera namdzoza Davide pomwepo akhale mfumu ya nyumba ya Yuda. Ndipo wina anauza Davide kuti, Anthu a ku Yabesi-Giliyadi ndiwo amene anamuika Saulo.


Ndipo Rizipa mwana wamkazi wa Aya anatenga chiguduli, nadziyalira ichi pathanthwe, kuyambira pakukolola kufikira madzi ochokera kumwamba adawagwera; ndipo sadalole mbalame za m'mlengalenga kutera pa iwo usana, kapena zilombo zakuthengo usiku.


Ndipo Davide ananka natenga mafupa a Saulo ndi mafupa a Yonatani mwana wake kwa anthu a ku Yabesi-Giliyadi amene anawaba m'khwalala la Beteseani, kumene Afilisti adawapachika, tsiku lija Afilistiwo anapha Saulo ku Gilibowa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa