2 Samueli 20:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anatuluka namtsata anthu a Yowabu, ndi Akereti ndi Apeleti, ndi anthu onse amphamvu; natuluka mu Yerusalemu kukalondola Sheba mwana wa Bikiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anatuluka namtsata anthu a Yowabu, ndi Akereti ndi Apeleti, ndi anthu onse amphamvu; natuluka m'Yerusalemu kukalondola Sheba mwana wa Bikiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Choncho Abisai uja, pamodzi ndi ankhondo a Yowabu, ndi Akereti, ndi Apeleti, ndi anyonga onse, adatuluka ku Yerusalemu kumalondola Sheba, mwana wa Bikiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kotero anthu a Yowabu, Akereti ndi Apeleti ndiponso asilikali onse amphamvu anapita motsogozedwa ndi Abisai. Iwo anayenda kuchokera ku Yerusalemu kuthamangitsa Seba mwana wa Bikiri. Onani mutuwo |