2 Samueli 20:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo Yowabu anali woyang'anira khamu lonse la Israele; ndi Benaya, mwana wa Yehoyada, anayang'anira Akereti ndi Apeleti; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo Yowabu anali woyang'anira khamu lonse la Israele; ndi Benaya, mwana wa Yehoyada, anayang'anira Akereti ndi Apeleti; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Yowabu ankalamulira gulu lonse lankhondo la Aisraele. Ndipo Benaya, mwana wa Yehoyada, ankalamulira Akereti ndi Apeleti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Yowabu ndiye amalamulira gulu lonse la ankhondo. Benaya mwana wa Yehoyada amalamulira Akereti ndi Apeleti. Onani mutuwo |