Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 20:24 - Buku Lopatulika

24 ndi Adoramu anayang'anira msonkho; ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 ndi Adoramu anayang'anira msonkho; ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Adoniramu anali mkulu woyang'anira za thangata. Yehosafati, mwana wa Ahiludi, anali mlembi wolemba mbiri ya dziko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Adoramu amayangʼanira anthu ogwira ntchito ya thangata, Yehosafati mwana wa Ahiludi anali mlembi wa zochitika,

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 20:24
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yowabu mwana wa Zeruya anayang'anira ankhondo, ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri,


Pamenepo mfumu Rehobowamu anatuma Adoramu wamsonkho, ndipo Aisraele onse anamponya miyala, nafa. Ndipo mfumu Rehobowamu anafulumira kulowa m'galeta wake kuthawira ku Yerusalemu.


Elihorefe ndi Ahiya ana a Sisa alembi, Yehosafati mwana wa Ahiludi wolembera mbiri,


ndi Ahisara anayang'anira banja la mfumu, ndi Adoniramu mwana wa Abida anali wamsonkho.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa