2 Samueli 20:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Yowabu anayankha nati, Iai ndi pang'ono ponse, chikhale kutali kwa ine, kuti ndingameze ndi kuononga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Yowabu anayankha nati, Iai ndi pang'ono ponse, chikhale kutali kwa ine, kuti ndingameze ndi kuononga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Yowabu adayankha kuti, “Iyai, ine sindikufuna konse kuwononga mzinda uno. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Yowabu anayankha kuti, “Ayi ndisatero. Ine sindikufuna kuwufafaniza kapena kuwuwononga. Onani mutuwo |