2 Samueli 20:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo iye analankhula, nati, Kale adanena kuti, Zoonadi adzapempha uphungu ku Abele; ndipo potero mlandu udatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo iye analankhula, nati, Kale adanena kuti, Zoonadi adzapempha uphungu ku Abele; ndipo potero mlandu udatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Apo mkazi uja adati, “Paja anthu kale ankati, ‘Kapempheni nzeru ku Abele.’ Nkhani zao ankazitha motero. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iye anapitiriza kunena kuti, “Kalekale ankanena kuti, ‘Kapeze yankho lako ku Abeli,’ ndipo nkhani imathera pamenepo. Onani mutuwo |