Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 2:28 - Buku Lopatulika

28 Chomwecho Yowabu anaomba lipenga, anthu onse naima, naleka kupirikitsa Aisraele, osaponyana naonso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Chomwecho Yowabu anaomba lipenga, anthu onse naima, naleka kupirikitsa Aisraele, osaponyana naonso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Choncho Yowabu adaliza lipenga, ndipo anthu onse adaleka, osathamangitsanso Aisraele, ndipo sadamenyane nawonso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Chomwecho Yowabu analiza lipenga, ndipo ankhondo onse anayima. Iwo analeka kuthamangitsa Aisraeli kapena kumenyana nawo.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 2:28
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Yowabu analiza lipenga, ndipo anthu anabwerera naleka kupirikitsa Aisraele; pakuti Yowabu analetsa anthuwo.


Yowabu nati, Pali Mulungu, iwe ukadapanda kunena, anthu akadabalalika m'mawa osatsata yense mbale wake.


Pomwepo mkaziyo anapita kwa anthu onse mwa nzeru yake. Ndipo iwo anadula mutu wa Sheba mwana wa Bikiri, nauponya kunja kwa Yowabu. Ndipo analiza lipenga, nabalalika kuchoka mumzindamo, munthu yense kunka ku hema wake. Ndipo Yowabu anabwerera kunka ku Yerusalemu kwa mfumu.


Ndipo panali nkhondo nthawi yaitali pakati pa nyumba ya Saulo ndi nyumba ya Davide. Koma Davide analimba chilimbire, ndi nyumba ya Saulo inafooka chifokere.


Ndipo Yonatani anathyola kaboma ka Afilisti lokhala ku Geba, ndipo Afilisti anamva za ichi. Ndipo Saulo analiza lipenga m'dziko monse, nati, Amve Ahebri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa