Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 2:29 - Buku Lopatulika

29 Ndipo Abinere ndi anthu ake anachezera usiku wonse kupyola chidikha, naoloka Yordani, napyola Bitroni lonse nafika ku Mahanaimu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Ndipo Abinere ndi anthu ake anachezera usiku wonse kupyola chidikha, naoloka Yordani, napyola Bitroni lonse nafika ku Mahanaimu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Choncho Abinere ndi anthu ake adayenda usiku wonse, nabzola chidikha cha Araba. Adaoloka mtsinje wa Yordani, ndipo adayenda m'maŵa monse, nakafika ku Mahanaimu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Usiku wonsewo Abineri ndi ankhondo ake anayenda kudutsa Araba. Iwo anawoloka Yorodani, napitirira mpaka kudutsa dera lonse la Bitironi ndipo anafika ku Mahanaimu.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 2:29
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yowabu anabwerera pakutsata Abinere. Ndipo pamene anasonkhanitsa pamodzi anthu onse anasowa anthu a Davide khumi ndi asanu ndi anai ndi Asahele.


Koma Abinere, mwana wa Nere, kazembe wa khamu la ankhondo a Saulo anatenga Isiboseti mwana wa Saulo, namuolotsa nanka naye ku Mahanaimu;


Koma polowa iwo m'nyumbamo iye ali chigonere pakama pake m'chipindamo, anamkantha, namupha namdula mutu wake, nautenga namuka njira ya kuchidikha usiku wonse.


Mpaka dzuwa litapepa, mithunzi ndi kutanimpha, bwera, bwenzi langawe, nukhale ngati mphoyo pena mwana wa mbawala pa mapiri a mipata.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa