2 Samueli 2:20 - Buku Lopatulika20 Pomwepo Abinere anacheuka nati, Kodi ndi iwe Asahele? Iye nayankha, Ndine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pomwepo Abinere anacheuka nati, Kodi ndi iwe Asahele? Iye nayankha, Ndine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono Abinere adacheuka nati, “Kodi ndiwe, Asahele?” Iye adayankha kuti, “Ndine amene.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Abineri anayangʼana mʼmbuyo ndipo anafunsa, “Kodi ndiwe Asaheli?” Iye anayankha kuti, “Ndine.” Onani mutuwo |