2 Samueli 2:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Asahele anapirikitsa Abinere. Ndipo m'kuthamanga kwake sanapatukire kulamanja, kapena kulamanzere, pakutsata Abinere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Asahele anapirikitsa Abinere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Iyeyo adathamangitsa Abinere. Pothamangapo sankayang'ana uku ndi uku, maso anali pa Abinere basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Iye anathamangitsa Abineri ndipo sanakhotere kumanja kapena kumanzere pamene amamutsatira. Onani mutuwo |