2 Samueli 2:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Davide anali mfumu ya nyumba ya Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziwiri kudza miyezi isanu ndi umodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Davide anali mfumu ya nyumba ya Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziwiri kudza miyezi isanu ndi umodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ndipo Davide adakhala mfumu ya fuko la Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziŵiri ndi theka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Davide anakhala mfumu ku Hebroni akulamulira fuko la Yuda, kwa zaka zisanu ndi chimodzi ndi miyezi isanu ndi umodzi. Onani mutuwo |