Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 2:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Davide anakhala mfumu ku Hebroni akulamulira fuko la Yuda, kwa zaka zisanu ndi chimodzi ndi miyezi isanu ndi umodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Ndipo Davide anali mfumu ya nyumba ya Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziwiri kudza miyezi isanu ndi umodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo Davide anali mfumu ya nyumba ya Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziwiri kudza miyezi isanu ndi umodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ndipo Davide adakhala mfumu ya fuko la Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziŵiri ndi theka.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 2:11
5 Mawu Ofanana  

Isi-Boseti mwana wa Sauli anali wa zaka makumi anayi pamene anakhala mfumu ya Israeli ndipo analamulira zaka ziwiri. Koma fuko la Yuda linatsatira Davide.


Iyeyo nʼkuti atalamulira Israeli kwa zaka makumi anayi. Ku Hebroni analamulira zaka zisanu ndi ziwiri ndipo ku Yerusalemu analamulira zaka 33.


Iye analamulira Israeli kwa zaka makumi anayi; zaka zisanu ndi ziwiri ali ku Hebroni ndi zaka 33 ali ku Yerusalemu.


Ana asanu ndi mmodzi awa a Davide anabadwira ku Hebroni kumene analamulirako zaka zisanu ndi ziwiri ndi miyezi isanu ndi umodzi. Davide analamuliranso mu Yerusalemu kwa zaka 33,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa