2 Samueli 19:34 - Buku Lopatulika34 Koma Barizilai ananena ndi mfumu, Masiku a zaka za moyo wanga ndiwo angati, kuti ndiyenera kukwera ndi mfumu kunka ku Yerusalemu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Koma Barizilai ananena ndi mfumu, Masiku a zaka za moyo wanga ndiwo angati, kuti ndiyenera kukwera ndi mfumu kunka ku Yerusalemu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Koma Barizilai adafunsa mfumu kuti, “Kodi ine zanditsalira zaka zingati zokhalabe moyo, kuti ndingapite nanu amfumu ku Yerusalemu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Barizilai anayankha mfumu kuti, “Kodi zakhala zaka zingati zoti ndikhale ndi moyo, kuti ndipite ku Yerusalemu ndi mfumu? Onani mutuwo |