2 Samueli 19:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo mfumu inanena ndi Barizilai, Tiyeni muoloke nane, ndipo ndidzakusungani pamodzi ndi ine ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo mfumu inanena ndi Barizilai, Tiyeni muoloke nane, ndipo ndidzakusungani pamodzi ndi ine ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Choncho mfumu idauza Barizilai kuti, “Tiye tipite limodzi, ndikakusunga ku Yerusalemu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Mfumu inati kwa Barizilai, “Woloka nane ndipo ukakhale ndi ine mu Yerusalemu ndipo ineyo ndidzakusamalira.” Onani mutuwo |