2 Samueli 19:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo Barizilai, Mgiliyadi anatsika kuchokera ku Rogelimu; nayambuka pa Yordani ndi mfumu, kuti akamuolotse pa Yordani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo Barizilai, Mgiliyadi anatsika kuchokera ku Rogelimu; nayambuka pa Yordani ndi mfumu, kuti akamuolotse pa Yordani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Tsono Barizilai Mgiliyadi adafika kuchokera ku Rogelimu. Adapita ndi mfumu mpaka ku Yordani kuti akaiperekeze pooloka Yordani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Barizilai Mgiliyadi anabweranso kuchokera ku Rogelimu kudzawoloka Yorodani ndi mfumu ndi kumuperekeza kuchokera kumeneko. Onani mutuwo |