2 Samueli 19:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo Mefiboseti anati kwa mfumu, Lingakhale lonselo alitenge, popeza mbuye wanga mfumu wabwera mumtendere kunyumba yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo Mefiboseti anati kwa mfumu, Lingakhale lonselo alitenge, popeza mbuye wanga mfumu wabwera mumtendere kunyumba yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Koma Mefiboseti adauza mfumu kuti, “Mloleni mnzangayu kuti atenge ndiye chuma chonsecho. Kwa ine kwakwana kuti inu mbuyanga mfumu mwafika kwanu kuno mwamtendere.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Mefiboseti anati kwa mfumu, “Muloleni atenge zonse, pakuti tsopano mbuye wanga mwafika kwanu mu mtendere.” Onani mutuwo |