2 Samueli 19:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo iye anandinamizira mnyamata wanu kwa mbuye wanga mfumu; koma mbuye wanga mfumu ali ngati mthenga wa Mulungu; chifukwa chake chitani chimene chikukomerani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo iye anandinamizira mnyamata wanu kwa mbuye wanga mfumu; koma mbuye wanga mfumu ali ngati mthenga wa Yehova; chifukwa chake chitani chimene chikukomerani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Koma iyeyo nkundisinjirira ine kapolo wanu kwa inu mbuyanga mfumu. Komatu inu muli ngati mngelo wa Mulungu. Nchifukwa chake tsono, muchite zimene zikukomereni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Ndipo wayankhula zosinjirira za ine mtumiki wanu kwa inu mbuye wanga mfumu. Mbuye wanga mfumu ali ngati mngelo wa Mulungu ndipo chitani chimene chikukomerani. Onani mutuwo |