2 Samueli 19:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo kunali pakufika iye ku Yerusalemu kukakomana ndi mfumu, mfumu inanena naye, Chifukwa ninji sunapite nane Mefiboseti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo kunali pakufika iye ku Yerusalemu kukakomana ndi mfumu, mfumu inanena naye, Chifukwa ninji sunapita nane Mefiboseti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ndiye pamene ankabwera ku Yerusalemu kudzakumana ndi mfumu, mfumuyo idamufunsa kuti, “Iwe Mefiboseti, chifukwa chiyani sudapite nane limodzi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pamene anafika kuchokera ku Yerusalemu kudzakumana ndi mfumu, mfumu inamufunsa kuti, “Nʼchifukwa chiyani sunapite nane Mefiboseti?” Onani mutuwo |