2 Samueli 19:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo mfumu inanena ndi Simei, Sudzafa. Mfumu nimlumbirira iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo mfumu inanena ndi Simei, Sudzafa. Mfumu nimlumbirira iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndipo mfumu idauza Simei kuti, “Ndikunenetsa molumbira kuti iwe Simei suphedwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndipo mfumu inati kwa Simei, “Iwe Simei suphedwa.” Ndipo mfumuyo inalonjeza ndi lumbiro. Onani mutuwo |