2 Samueli 19:21 - Buku Lopatulika21 Koma Abisai mwana wa Zeruya anayankha nati, Kodi sadzaphedwapo Simei chifukwa cha kutemberera wodzozedwa wa Yehova? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma Abisai mwana wa Zeruya anayankha nati, Kodi sadzaphedwapo Simei chifukwa cha kutemberera wodzozedwa wa Yehova? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pompo Abisai, mwana wa Zeruya, adafunsa kuti, “Kodi Simeiyu ndiye saphedwa chifukwa chotukwana wodzozedwa wa Chauta?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndipo Abisai mwana wa Zeruya anati, “Kodi Simei saphedwa chifukwa cha ichi? Iye anatukwana wodzozedwa wa Yehova.” Onani mutuwo |