2 Samueli 19:19 - Buku Lopatulika19 Nati kwa mfumu, Mbuye wanga asandiwerengere ine mphulupulu ndiponso musakumbukire chimene mnyamata wanu ndinachita mwamphulupulu tsiku lija mbuye wanga mfumu anatuluka ku Yerusalemu, ngakhale kuchisunga mumtima mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Nati kwa mfumu, Mbuye wanga asandiwerengere ine mphulupulu ndiponso musakumbukire chimene mnyamata wanu ndinachita mwamphulupulu tsiku lija mbuye wanga mfumu anatuluka ku Yerusalemu, ngakhale kuchisunga mumtima mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Adauza mfumu kuti, “Mbuyanga, chonde mundikhululukire, musakumbukirenso tchimo limene ine kapolo wanu ndidachita pa tsiku lija, pamene inu mbuyanga mfumu munkachoka mu Yerusalemu. Amfumu musazisunge kukhosi zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 ndipo anati, “Mbuye wanga musaganizire za kulakwa kwanga. Musakumbukire zolakwa zimene mtumiki wanu anakuchitirani tsiku limene mbuye wanga mfumu mumachoka mu Yerusalemu. Mfumu musazikumbukirenso zimenezi. Onani mutuwo |