2 Samueli 19:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Simei, mwana wa Gera, Mbenjamini, wa ku Bahurimu, anafulumira natsika pamodzi ndi anthu a Yuda kuti akakomane ndi mfumu Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Simei, mwana wa Gera, Mbenjamini, wa ku Bahurimu, anafulumira natsika pamodzi ndi anthu a Yuda kuti akakomane ndi mfumu Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono Simei, mwana wa Gera, Mbenjamini wa ku Bahurimu, adabwera mofulumira pamodzi ndi Ayuda kudzakumana ndi mfumu Davide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Simei mwana wa Gera, wa fuko la Benjamini wa ku Bahurimu, anabwera mofulumira pamodzi ndi Ayuda kudzakumana ndi mfumu Davide. Onani mutuwo |