2 Samueli 19:15 - Buku Lopatulika15 Chomwecho mfumu inabwera nifika ku Yordani. Ndipo Ayuda anadza ku Giligala, kuti akakomane ndi mfumu, ndi kumuolotsa mfumu pa Yordani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Chomwecho mfumu inabwera nifika ku Yordani. Ndipo Ayuda anadza ku Giligala, kuti akakomane ndi mfumu, ndi kumuolotsa mfumu pa Yordani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Motero mfumu idabwerera ku Yordani. Ndipo anthu onse a mtundu wa Yuda adafika ku Giligala kudzakumana ndi mfumu ndi kuiwolotsa Yordani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kotero mfumu inabwerera ndipo inakafika mpaka ku Yorodani. Tsono anthu a ku Yuda anabwera ku Giligala kuti akakumane ndi mfumu ndi kumuwolotsa Yorodani. Onani mutuwo |